Maliko 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu akukwera ngalawa, munthu amene anali ndi ziwanda uja anamuchonderera kuti apite nawo.+
18 Ndiyeno Yesu akukwera ngalawa, munthu amene anali ndi ziwanda uja anamuchonderera kuti apite nawo.+