Maliko 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho munthu uja anachoka ndipo anayamba kufalitsa mu Dekapoli* zonse zimene Yesu anamuchitira, moti anthu onse anadabwa kwambiri. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:20 Yesu—Ndi Njira, tsa. 115 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 27
20 Choncho munthu uja anachoka ndipo anayamba kufalitsa mu Dekapoli* zonse zimene Yesu anamuchitira, moti anthu onse anadabwa kwambiri.
5:20 Yesu—Ndi Njira, tsa. 115 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 27