Maliko 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, gulu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, pa nthawiyi iye anali mʼmphepete mwa nyanja.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:21 Yesu—Ndi Njira, tsa. 116
21 Yesu atawolokanso pangalawa kubwerera kutsidya lina, gulu lalikulu la anthu linasonkhana kwa iye, pa nthawiyi iye anali mʼmphepete mwa nyanja.+