Maliko 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Madokotala ambiri anamuchititsa kuti avutike kwambiri.* Iye anawononga chuma chake chonse koma sanachire, mʼmalomwake matendawo ankangokulirakulira.
26 Madokotala ambiri anamuchititsa kuti avutike kwambiri.* Iye anawononga chuma chake chonse koma sanachire, mʼmalomwake matendawo ankangokulirakulira.