Maliko 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atamva zokhudza Yesu, anakalowa mʼgulu la anthulo nʼkumudzera kumbuyo kwake, kenako anagwira malaya ake akunja.+
27 Atamva zokhudza Yesu, anakalowa mʼgulu la anthulo nʼkumudzera kumbuyo kwake, kenako anagwira malaya ake akunja.+