Maliko 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nthawi yomweyo, Yesu anazindikira kuti mphamvu+ yatuluka mʼthupi mwake ndipo anatembenuka mʼgulu la anthulo nʼkufunsa kuti: “Ndi ndani wagwira malaya anga akunjawa?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:30 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 116 Nsanja ya Olonda,6/1/1987, tsa. 25
30 Nthawi yomweyo, Yesu anazindikira kuti mphamvu+ yatuluka mʼthupi mwake ndipo anatembenuka mʼgulu la anthulo nʼkufunsa kuti: “Ndi ndani wagwira malaya anga akunjawa?”+
5:30 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 116 Nsanja ya Olonda,6/1/1987, tsa. 25