-
Maliko 5:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Mayi uja anachita mantha nʼkuyamba kunjenjemera atadziwa zimene zamuchitikira ndipo anafika pafupi nʼkugwada pamaso pake nʼkumuuza zoona zonse.
-