Maliko 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma Yesu anamva zimene ankanenazo ndipo anauza mtsogoleri wa sunagogeyo kuti: “Usaope, ingokhala ndi chikhulupiriro basi.”+
36 Koma Yesu anamva zimene ankanenazo ndipo anauza mtsogoleri wa sunagogeyo kuti: “Usaope, ingokhala ndi chikhulupiriro basi.”+