-
Maliko 5:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kumuseka monyoza. Koma atawatulutsa onsewo, anatenga bambo ndi mayi a mwanayo komanso anthu amene anali naye aja, ndipo analowa kumene kunali mwanayo.
-