-
Maliko 5:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Nthawi yomweyo mtsikanayo anadzuka nʼkuyamba kuyenda. (Mtsikanayo anali ndi zaka 12.) Ndipo anthuwo anasangalala kwambiri.
-