Maliko 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo, ngakhale ndi achibale ake, ngakhale mʼnyumba mwake momwe, koma kwina.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:4 Yesu—Ndi Njira, tsa. 121 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, tsa. 8
4 Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo, ngakhale ndi achibale ake, ngakhale mʼnyumba mwake momwe, koma kwina.”+