Maliko 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anaitana ophunzira ake 12 aja nʼkuyamba kuwatumiza awiriawiri+ ndipo anawapatsa mphamvu kuti azitha kutulutsa mizimu yonyansa.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1987, ptsa. 26-27
7 Kenako anaitana ophunzira ake 12 aja nʼkuyamba kuwatumiza awiriawiri+ ndipo anawapatsa mphamvu kuti azitha kutulutsa mizimu yonyansa.+