Maliko 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso anawalamula kuti asatenge kanthu pa ulendowo koma ndodo yokha basi. Anawalamula kuti asatenge mkate, thumba la chakudya kapena ndalama* mʼzikwama zawo,+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:8 Nsanja ya Olonda,3/15/2011, tsa. 67/15/1987, tsa. 27
8 Komanso anawalamula kuti asatenge kanthu pa ulendowo koma ndodo yokha basi. Anawalamula kuti asatenge mkate, thumba la chakudya kapena ndalama* mʼzikwama zawo,+