Maliko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Mfumu Herode inamva zimenezi chifukwa dzina la Yesu linatchuka kwambiri ndipo anthu ankanena kuti: “Yohane Mʼbatizi wauka kwa akufa nʼchifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+
14 Ndiyeno Mfumu Herode inamva zimenezi chifukwa dzina la Yesu linatchuka kwambiri ndipo anthu ankanena kuti: “Yohane Mʼbatizi wauka kwa akufa nʼchifukwa chake akuchita ntchito zamphamvu.”+