Maliko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ananena zimenezi chifukwa Herodeyo anatumiza anthu kuti akagwire Yohane nʼkumumanga ndipo anamutsekera mʼndende chifukwa cha Herodiya, mkazi wa mchimwene wake Filipo amene Herodeyo anakwatira.+
17 Ananena zimenezi chifukwa Herodeyo anatumiza anthu kuti akagwire Yohane nʼkumumanga ndipo anamutsekera mʼndende chifukwa cha Herodiya, mkazi wa mchimwene wake Filipo amene Herodeyo anakwatira.+