Maliko 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anachita zimenezi chifukwa Yohane ankauza Herode kuti: “Nʼzosaloleka kuti mutenge mkazi wa mchimwene wanu.”+
18 Anachita zimenezi chifukwa Yohane ankauza Herode kuti: “Nʼzosaloleka kuti mutenge mkazi wa mchimwene wanu.”+