Maliko 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Herode ankaopa Yohane chifukwa ankadziwa kuti ndi munthu wolungama komanso woyera,+ choncho ankamuteteza. Atamva zimene ankanena anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mosangalala.
20 Herode ankaopa Yohane chifukwa ankadziwa kuti ndi munthu wolungama komanso woyera,+ choncho ankamuteteza. Atamva zimene ankanena anathedwa nzeru, komabe anapitiriza kumumvetsera mosangalala.