Maliko 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno tsiku loti Herodiya akwaniritse zolinga zake linafika. Limeneli linali tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode+ ndipo anakonzera chakudya chamadzulo nduna zake, akuluakulu a asilikali ndi anthu otchuka kwambiri a mu Galileya.+
21 Ndiyeno tsiku loti Herodiya akwaniritse zolinga zake linafika. Limeneli linali tsiku lokumbukira kubadwa kwa Herode+ ndipo anakonzera chakudya chamadzulo nduna zake, akuluakulu a asilikali ndi anthu otchuka kwambiri a mu Galileya.+