-
Maliko 6:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiye mwana wamkazi wa Herodiya analowa nʼkuyamba kuvina, moti anasangalatsa Herode ndi ena amene ankadya naye limodzi. Tsopano mfumu inauza mtsikanayo kuti: “Undipemphe chilichonse chimene ukufuna ndipo ndikupatsa.”
-