-
Maliko 6:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndithu, anachita kumulumbirira kuti: “Chilichonse chimene ungandipemphe ndikupatsa, ngakhale hafu ya ufumu wangawu.”
-