-
Maliko 6:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho anatuluka nʼkukafunsa mayi ake kuti: “Ndikapemphe chiyani?” Mayi akewo anamuuza kuti: “Kapemphe mutu wa Yohane Mʼbatizi.”
-