Maliko 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngakhale kuti mfumu inamva chisoni kwambiri, sinafune kumukanira poganizira lumbiro lake lija komanso alendo ake aja.*
26 Ngakhale kuti mfumu inamva chisoni kwambiri, sinafune kumukanira poganizira lumbiro lake lija komanso alendo ake aja.*