-
Maliko 6:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho, nthawi yomweyo mfumu inatumiza msilikali amene ankamulondera nʼkumulamula kuti abweretse mutu wa Yohane. Iye anapita nʼkukamudula mutu mundendemo
-