Maliko 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano kunja kunayamba kuda ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye nʼkunena kuti: “Kuno nʼkopanda anthu ndipo nthawi yatha.+
35 Tsopano kunja kunayamba kuda ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye nʼkunena kuti: “Kuno nʼkopanda anthu ndipo nthawi yatha.+