Maliko 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.” Yesu atanena zimenezi iwo anamufunsa kuti: “Kodi tipite kukagula mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari* 200 nʼkuipereka kwa anthuwa kuti adye?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:37 Yesu—Ndi Njira, tsa. 128 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, ptsa. 16-1710/15/1986, tsa. 21
37 Koma iye anawayankha kuti: “Inuyo muwapatse chakudya.” Yesu atanena zimenezi iwo anamufunsa kuti: “Kodi tipite kukagula mitanda ya mkate ya ndalama zokwana madinari* 200 nʼkuipereka kwa anthuwa kuti adye?”+