Maliko 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina loyangʼanizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+
45 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina loyangʼanizana nalo cha ku Betsaida. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+