Maliko 6:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Ndipo akangolowa mʼmidzi kapena mʼmizinda komanso mʼmadera ozungulira, anthu ankakhazika odwala mʼmisika. Iwo ankamuchonderera kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachira. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:56 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 16
56 Ndipo akangolowa mʼmidzi kapena mʼmizinda komanso mʼmadera ozungulira, anthu ankakhazika odwala mʼmisika. Iwo ankamuchonderera kuti angogwira ulusi wopota wamʼmphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo anthu onse amene anaugwira anachira.