Maliko 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atasamba. Pali miyambo inanso yambiri imene anailandira ndipo akuitsatira, monga kuviika mʼmadzi makapu, mitsuko ndi ziwiya zakopa.*)+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Nsanja ya Olonda,6/15/1997, tsa. 1310/15/1989, tsa. 311/15/1989, tsa. 11
4 Ndipo akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atasamba. Pali miyambo inanso yambiri imene anailandira ndipo akuitsatira, monga kuviika mʼmadzi makapu, mitsuko ndi ziwiya zakopa.*)+