Maliko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawayankha kuti: “Yesaya analosera zolondola zokhuza anthu achinyengo inu, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti, ‘Anthu awa amandilemekeza ndi milomo yokha, koma mitima yawo aiika kutali ndi ine.+
6 Iye anawayankha kuti: “Yesaya analosera zolondola zokhuza anthu achinyengo inu, mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti, ‘Anthu awa amandilemekeza ndi milomo yokha, koma mitima yawo aiika kutali ndi ine.+