Maliko 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu,’+ komanso anati, ‘Aliyense wolankhula mawu achipongwe kwa bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.’+
10 Mwachitsanzo, Mose ananena kuti, ‘Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu,’+ komanso anati, ‘Aliyense wolankhula mawu achipongwe kwa bambo ake kapena mayi ake aziphedwa.’+