Maliko 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mukamachita zimenezi, mumapangitsa kuti mawu a Mulungu akhale opanda pake chifukwa cha miyambo yanu imene munaipereka kwa anthu.+ Ndipo mumachita zinthu zambiri ngati zimenezi.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Nsanja ya Olonda,12/1/1988, ptsa. 4-56/1/1987, tsa. 14
13 Mukamachita zimenezi, mumapangitsa kuti mawu a Mulungu akhale opanda pake chifukwa cha miyambo yanu imene munaipereka kwa anthu.+ Ndipo mumachita zinthu zambiri ngati zimenezi.”+