Maliko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu nʼkulowa mʼthupi mwake chimene chingaipitse munthu. Koma zinthu zimene zimatuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+
15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu nʼkulowa mʼthupi mwake chimene chingaipitse munthu. Koma zinthu zimene zimatuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+