Maliko 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano atalowa mʼnyumba ina kutali ndi gulu la anthulo, ophunzira ake anayamba kumufunsa za fanizo lija.+
17 Tsopano atalowa mʼnyumba ina kutali ndi gulu la anthulo, ophunzira ake anayamba kumufunsa za fanizo lija.+