-
Maliko 7:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho iye anawafunsa kuti: “Kodi nanunso ndinu osazindikira ngati iwo aja? Kodi simukudziwa kuti palibe chochokera kunja kwa thupi nʼkulowa mʼthupi mwa munthu chimene chingamuipitse?
-