-
Maliko 7:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Zili choncho chifukwa sichidutsa mumtima mwake koma mʼmatumbo mwake, ndipo chimakatuluka kuchimbudzi.” Ndi mawu amenewa Yesu anagamula kuti zakudya zonse nʼzoyera.
-