Maliko 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zachigololo, dyera, kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lopanda manyazi,* diso la kaduka, mawu onyoza, kudzikweza ndiponso kuchita zinthu mopanda nzeru.
22 zachigololo, dyera, kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lopanda manyazi,* diso la kaduka, mawu onyoza, kudzikweza ndiponso kuchita zinthu mopanda nzeru.