Maliko 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atachoka kumeneko anapita mʼchigawo cha Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa mʼnyumba ina ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 Nsanja ya Olonda,11/15/1987, tsa. 8
24 Atachoka kumeneko anapita mʼchigawo cha Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa mʼnyumba ina ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe.