Maliko 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nthawi yomweyo, mayi wina amene mwana wake wamkazi anagwidwa ndi mzimu wonyansa anamva za iye ndipo anabwera nʼkudzagwada pamapazi ake.+
25 Nthawi yomweyo, mayi wina amene mwana wake wamkazi anagwidwa ndi mzimu wonyansa anamva za iye ndipo anabwera nʼkudzagwada pamapazi ake.+