-
Maliko 7:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Mayiyu anali Mgiriki, wa Chisurofoinike. Iye anapempha Yesu mobwerezabwereza kuti atulutse chiwanda mwa mwana wakeyo.
-