Maliko 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho anapita kunyumba kwake ndipo anakapeza mwanayo atagona pabedi chiwandacho chitatuluka.+