Maliko 7:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamene Yesu ankachoka mʼchigawo cha Turo kupita kunyanja ya Galileya, anadutsa ku Sidoni komanso mʼchigawo cha Dekapoli.*+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:31 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda,11/15/1987, tsa. 9
31 Pamene Yesu ankachoka mʼchigawo cha Turo kupita kunyanja ya Galileya, anadutsa ku Sidoni komanso mʼchigawo cha Dekapoli.*+