Maliko 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anamubweretsera munthu wa vuto losamva komanso wovutika kulankhula.+ Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.
32 Kumeneko anthu anamubweretsera munthu wa vuto losamva komanso wovutika kulankhula.+ Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.