Maliko 7:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atatero, makutu ake anatseguka+ ndipo vuto lake losalankhulalo linatheratu, moti anayamba kulankhula bwinobwino.
35 Atatero, makutu ake anatseguka+ ndipo vuto lake losalankhulalo linatheratu, moti anayamba kulankhula bwinobwino.