Maliko 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimene zinachitikazo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, mʼpamenenso iwo ankazifalitsa kwambiri.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:36 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, tsa. 28
36 Ndiyeno anawalamula kuti asauze aliyense zimene zinachitikazo.+ Koma ankati akawaletsa mwamphamvu kuti asauze aliyense, mʼpamenenso iwo ankazifalitsa kwambiri.+