Maliko 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inde, iwo anadabwa kwambiri+ ndipo ananena kuti: “Wachita zinthu zonse bwinobwino ndithu. Ngakhale anthu amene anali ndi vuto losamva akumva komanso amene anali ndi vuto losalankhula akulankhula.”+
37 Inde, iwo anadabwa kwambiri+ ndipo ananena kuti: “Wachita zinthu zonse bwinobwino ndithu. Ngakhale anthu amene anali ndi vuto losamva akumva komanso amene anali ndi vuto losalankhula akulankhula.”+