-
Maliko 8:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Yesu ataona zimenezo, anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukukangana pa nkhani yosowa mkate? Kodi simukuzindikira ndi kumvetsa tanthauzo lake mpaka pano? Kodi mitima yanu ikadali yosazindikira?
-