Maliko 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 zimene zinachitika nditanyemanyema mitanda 5 ya mkate+ nʼkudyetsa amuna 5,000? Kodi munatolera madengu angati a zotsala?” Iwo anayankha kuti: “Anali madengu 12.”+
19 zimene zinachitika nditanyemanyema mitanda 5 ya mkate+ nʼkudyetsa amuna 5,000? Kodi munatolera madengu angati a zotsala?” Iwo anayankha kuti: “Anali madengu 12.”+