-
Maliko 8:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iye anagwiranso mʼmaso mwa munthuyo ndipo anayamba kuona bwinobwino. Munthuyo anachiriratu moti anayamba kuona chilichonse bwinobwino.
-