Maliko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atamva zimenezi, Yesu anatembenuka nʼkuyangʼana ophunzira ake, kenako anadzudzula Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga, Satana! Chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu, koma maganizo a anthu.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:33 Tsanzirani, tsa. 192 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 2710/15/2008, tsa. 25
33 Atamva zimenezi, Yesu anatembenuka nʼkuyangʼana ophunzira ake, kenako anadzudzula Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga, Satana! Chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu, koma maganizo a anthu.”+