Maliko 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa aliyense wochita manyazi ndi ine komanso mawu anga mu mʼbadwo wachigololo* ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:38 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, ptsa. 13-141/1/1990, tsa. 13
38 Chifukwa aliyense wochita manyazi ndi ine komanso mawu anga mu mʼbadwo wachigololo* ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzabwera mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+